Friday, October 27, 2006

 

Sad News to SDA Members

"Good beginning, bad ending of this day to all SDA members". This is coz their trip to Bunda College ya za Ulimi has been blocked by the VC's demand for K110,000.

These guys have been preparing for this trip mwinanso for the whole of this week, only to be cancelled out by the bigman himself after some stupid pieces of advise from his woman and his girlova may be.

Ena mwa mamembawa amakonzekera zokumana ndi matchiki awo, koma awotcha basi. Azikazi awo a kubundawo agona opanda ma panti kukonzekera ntchito ndi ma guy a ku Mzuni koma nawonso awotcha basi. Tizibwezi tawoto tagona to nkhanyula-nkhanyulatu, ndangomva poti "zikachitika mumvera kwa ife".

Kodi VeeCeeyo watani? Mwina poti ka chibwenzikake kaja ndika mpingo wina. Koma kamwana kamenekaja kamafuna chani kwa mdala ngati uja? "Maonekedwe apusisaeti!, kakungomupusisisatu wa forestry uja! Ine ndimadabwa kuti kamakonda kuvala mwa chizimayi, kamafuna kupikisana ndi mrs veecee eti!" Mwinaso sikanawinetu nthawi ijatu!

Comments: Post a Comment



<< Home

This page is powered by Blogger. Isn't yours?