Wednesday, April 05, 2006
Black ninjas and musu ninjas
We do not know if the standards have gone down or what the cause of 96 people writing supp is.
Maybe people were so busy with kugonana they did not have time for their books.
Nanga nchani? How can we have 96 as the number of Mzekezekes?
Before i forget, if you just join the mzekezekes during lunch or supper you might think that musu is up to something kuti mwina they've come for a meeting. A good number of them. Deferred exams? Why am i thinking otherwise?
Use condoms everytime you want to have sex. The fact that someone is at a University does not prevent them from being HIV positive.

Comments:
<< Home
often times we want to attribute our failures to other people. commenting on WHY 96 ninjas...it is not that the courses have gotten tougher, lecturer lazier, stricter or even genetic disposition..... No its not!!
we used to have people that were determined to pass when I was there. today it makes me sad.... what wrong with the attitude of the youth of today?
why is it that now youth just want to be ordinary, why not extra ordinary?why aiming for a 45%....
we used to have people who would solva maths kumakalasi usiku wonse kukuzizilatu... mpakana a bade kumawona ngati ukuwa playa!... munawothelapo iron inu!kukuwona ku Mzuni kekecha( ulipa desk by the way)..anthu kudwala after missing the dean's list....
Ambition osati zibwana ayi...people that were determined to make their own name not live in other people's shadows..
your future is in your hands. belive me what you do within the gates of Mzuni will haunt you forever!!!!

NO MORE CHAMPIONS THIS SEMESTER
eeeeeeeh! Mwakonzekera inu mufoira Champions yalephereka poti yaro ikubwerayi iwuzidwiratu chilungamo! nonse amene munamenya champions mutisiyire enafe timenye nawo world cup!
A Kho chonde mutisiyire mukufuna tidzichita kupelekeza madona athu kuli kukuopani kuti mutilanda???????????????????????????????
Ayi yaro ikubwerayi nde tikukhobolani fast!
Kuli edzi edzi kuli edzi edzi edzi eeeeeeeeeh! samala mayendedwe! Kuli ma Konti iwe yaro samara mayendedwe
Yaro woyeee! ma Kontinso woyeeeeeeeeeeeeee! Enanu mwina mugwire ma nurse wa

"Kho Kho Kho" Ulu ndi kulira kwa makina osokera zovala za ma Yaro akubwerawa!
Ge! ge! kukhapana chifukwa cha mayaro!, kodi akulu a magalasi aja adapulumuka ku mkwiyo wa a Pulezi..? Mkuluyo koma, aaa! Khini kodi?"
Kodi ada aja ayamba kumanga sisi chifukwa cha impea..t? He hede! Wina asoma chaka chake ndi chino.

When we remember last semesters events we think of laughing mwinanso nkusapula nazoso! Imagine" I didn't say you are stupid, I said you or I are stupid!"-mu hall!
"Maye maye maye! mesho lero uwonerela!Mesa siukufuna kudya exodos!"-Ku kandaha
Post a Comment